
Pasuwa asiya bwanji osewera ofunikira, aMalawi adabwa
Anthu ambiri m’masamba anchezo akuthera mawu mphunzitsi wa timu ya miyendo ya dziko lino ya Flames, Calisto Pasuwa kamba kosiya osewera ena pa mndandanda wa omwe akuyenera kutenga gawo pa masewero odzipezera malo mu mpikisano wa dziko lonse (World Cup) …